Chibompi

Crispy Malawi, Ayo Landie, BeatsByNice

[Intro]
It's Nice it's Nice
Mmh Baby mmh come on
Mmh baby
Ayo Landie
Mmh Mmh mwana salira (ay-ay, ay-ay)
Mmh Mmh mwana (ay-ay, ay-ay) salira (Okay-Okay)
Ufuna chani? hmm?

[Chorus]
Chibhompi (Uh-huh, uh-huh)
Mwana akufuna chibhompi (Uh-huh)
Mwana akufuna chibhompi (ukufuna chani huh?)
Mwana akufuna chibhompi
Nditha kupatsa chimodzi, bola usayambe kudya dothi
Vuto lake kukupatsa Chibhompi, uyamba kundipatsa chikondi

[Verse 1]
Nde ana ija mafunso ngati uli court
Nali busy kufotokoza zoti "mene umandiwonera muja ineyo tingatayane"
"Iwe chibhompi cha ulere inuyo mungagawane hee?"
Tanena "A" eh Tananena "E" ah wawona?
Nde uziti zandibanda ndikangoyamba kukhafa?
Tiye kubafa yama lover (Uh-Uh-Uh) (mmh-hm-mmh-hm)

[Chorus]
Chibhompi (mmh hm)
Mwana akufuna chibhompi (ukufuna chani huh?)
Mwana akufuna chibhompi
Mwana akufuna chibhompi
Nditha kupatsa chimodzi, bola usayambe kudya dothi
Vuto lake kukupatsa chibhompi, uyamba kundipatsa chikondi

[Verse 2]
Ine kuyiwala zoti ndili ndi mwana man (umatani?)
Kuyamba kukamba zaku Kanakan[?] (Zachamba eti)
Boys kundithila no fireman
Nangotaya man ndili ndi ma man
Ati "SPE usamakonde kusuta chonchi"
Ndampatsa ya banana flavour yapa couch
Nde mix ana amakonda ntochi kamba puff ndi chibhompi

[Chorus]
Hmm
Chibhompi (Uh-uh-uh)
Mwana akufuna chibhompi (akufuna chibhompi mwanayi)
Chibhompi (Uh-huh)
Mwana akufuna chibhompi (Uh-huh uh-huh)
Nditha kupatsa chimodzi (Eko Eko) bola usayambe kudya dothi
Vuto lake kukupatsa chibhompi uyamba kundipatsa chikondi
Chibhompi (Uh-huh)
Mwana akufuna chibhompi
'Mwana akufuna chibhompi
Mwana akufuna chibhompi (tontholola)

[Outro]
Mwana salira
Eko chibhompi
Eko
We ain't got no time
Mwana wabwino
Mwana wabwino

Curiosidades sobre la música Chibompi del Crispy Malawi

¿Cuándo fue lanzada la canción “Chibompi” por Crispy Malawi?
La canción Chibompi fue lanzada en 2024, en el álbum “DND”.
¿Quién compuso la canción “Chibompi” de Crispy Malawi?
La canción “Chibompi” de Crispy Malawi fue compuesta por Crispy Malawi, Ayo Landie, BeatsByNice.

Músicas más populares de Crispy Malawi

Otros artistas de