Koma Boys

Crispy Malawi, Krazie G, Ace Dirty, Nihilo (Producer), ChuxTpat$ePlan

[Intro: Crispy Malawi]
Koma boys
Ayo Nihilo bring the beat son haha
Zomwe imapanga boys ina
Isakuone ukuvina
Koma ukulira
(Hihihhihi)

[Chorus: Crispy Malawi]
Kundibela lighter ntakubanditsa (Aah) (Koma boys)
Kundibela phone ntakuyakitsa (Aah) (Koma boys)
Pamaso kuchiller kumbali Ku disser (Aah) (Koma boys)
Kubwera pa den kundikalipitsa(aah) (Koma boys)
Tisamavetsana kuwawa
Tizimvetsana kukoma boys
Kuyikana mkati
Osakankhirana mpaka Ku khoma boys
Kumagawanako wezi wezi
Osamaphangira boys
Slow paced kuvaya Ku front
(Tsitsa Pang'ono)
Osathamangira boys

[Verse 1 :Ace Dirty & (Crispy Malawi)]
Kundikweza kuzanditsitsa
Mbiri yanga mumayipitsa
Mumafuna zabwino zonse zikhale zanu
Mukuwona moyo
Kumandiyenda mbali ngati nkhanu
Kumbali muku hater pamaso kumandisamala
Kufuna kulanda mkazi wanga (koma boys)
Kundiponda Ka dollar kanga (koma boys)
Osakapeza kamtima mumafuna zoyambana
Pano ukupanga zanga
Pano tinadana

[Verse 2: Krazie G & Crispy Malawi]
Krazie tsitsi lako walitani?
Ukubanda grade yanji?
Ma trainer ngati njanji
Ungobanda Zi mbanji (Zi m'banji)
Kwa chigulu changa ine ndina lonjeza
Tizizangoyaka Ku chaser ndi kombeza
Kona drip yanga ikuteletele
Tele tele
Tele tele yeahhh
(Koma boys)

[Chorus: Crispy Malawi]
Kundibela lighter ntakubanditsa (Aah) (Koma boys)
Kundibela phone ntakuyakitsa (Aah) (Koma boys)
Pamaso kuchiller kumbali Ku disser (Koma boys)
Kubwera pa den kundikalipitsa (Aah) (Koma boys)
Tisamavetsana kuwawa
Tizimvetsana kukoma boys
Kuyikana mkati
Osakankhirana mpaka Ku khoma boys
Kumagawanako wezi wezi
Osamaphangira boys
Slow paced kuvaya Ku front
Osathamangira boys

[Outro: Crispy Malawi]
Zomwe imayithoka boys
Anyway osamafooka boys
Tizakukoka ma balls
Kukakuponya Ku falls
(Zomwe imapanga boys ina)
(Isakuone ukuvina)
(Koma ukulira)
(Koma boysss)
(Koma boysss)

Curiosidades sobre la música Koma Boys del Crispy Malawi

¿Cuándo fue lanzada la canción “Koma Boys” por Crispy Malawi?
La canción Koma Boys fue lanzada en 2023, en el álbum “MLW Tape II”.
¿Quién compuso la canción “Koma Boys” de Crispy Malawi?
La canción “Koma Boys” de Crispy Malawi fue compuesta por Crispy Malawi, Krazie G, Ace Dirty, Nihilo (Producer), ChuxTpat$ePlan.

Músicas más populares de Crispy Malawi

Otros artistas de