Nice Watch

Crispy Malawi, Krazie G, Crack Mapiri, Brainlock T-Kas

[Intro: Crispy Malawi]
Ayo Crack Mmh, hm
Mapiri

[Chorus: Crispy Malawi]
Ndikuna money ukufuna cha?
Ndikupita Konko umawopa cha?
Kusaka kwacha, Kukacha
Kusintha dollar ndi mpasha
Ndikufuna million, Sizongosintha Chameleon
Kwayaka moto ngati ifeyo tiliko
Siwe dolo ngati ifeyo tilipo

[Verse 1 : Krazie G & Crispy Malawi & (Brainlock T-Kas)]
"Sips Tea"
I mean look at the longevity
Afana opita sitisowa Tpt
Sound yokhonza koma ili pa repeat
Iwe tangochecker lyric
You can bet on me kuti usang'ambe ticket
Tavutitsaso South ngati Ama Kip Kip
Koma discipline ngati ndili Mzikiti
Nde osadabwa ndikaiphula
Mkazi wanga ndi dollar ndamutchula
Wako kungopeza dollar titha kumugula
Bars ya ine ndi homie bolaso Maula (Yeah)

[Bridge : Krazie G & (Brainlock T-Kas)]
More life, more shots (More shots)
Good Times (Good Times), Nice Watch (Nice Watch)
Blessings got a whole lot (Whole lot)
Blessings got a whole lot (Whole lot)

[Verse 2 : Crispy Malawi, Krazie G & (Brainlock T-Kas)]
More love, Less hate (Mmh)
Ndili ndi ma goals (Mmh), ngati golo (Mmh)
Kuvunga Round two, two ngati Folo (Yea)
Nde ndizingoyimba ngati ndapanga mtolo (Trap, Trap, Trap)
What a sight when she wine (Yea)
Dynamite I'm tryna make her mine (Mh, Mh)
What a sight when she- (Eh eh) Ndingofuna good vibes

[Chorus: Crispy Malawi]
Ndikuna money ukufuna cha?
Ndikupita Konko Umawopa cha?
Kusaka kwacha Kukacha
Kusintha dollar ndi mpasha
Ndikufuna million, Sizongosintha Chameleon
Kwayaka moto ngati ifeyo tiliko
Siwe dolo ngati ifeyo tilipo

Otros artistas de